Masalimo 71:10 - Buku Lopatulika10 Pakuti adani anga alankhula za ine; ndipo iwo akulalira moyo wanga apangana upo, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Pakuti adani anga alankhula za ine; ndipo iwo akulalira moyo wanga apangana upo, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Adani anga amandinena, anthu olondalonda moyo wanga amapangana limodzi, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Pakuti adani anga ayankhula motsutsana nane; iwo amene amadikira kuti andiphe amapangana pamodzi. Onani mutuwo |