Masalimo 66:2 - Buku Lopatulika2 Imbirani ulemerero wa dzina lake; pomlemekeza mumchitire ulemerero. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Imbirani ulemerero wa dzina lake; pomlemekeza mumchitire ulemerero. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Imbani nyimbo zoyamika dzina lake laulemerero, mumtamande mwaulemu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Imbani ulemerero wa dzina lake; kumutamanda kwake kukhale kwaulemerero. Onani mutuwo |