Masalimo 27:2 - Buku Lopatulika2 Pondifika ine ochita zoipa kudzadya mnofu wanga, inde akundisautsa ndi adani anga, anakhumudwa iwo nagwa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Pondifika ine ochita zoipa kudzadya mnofu wanga, inde akundisautsa ndi adani anga, anakhumudwa iwo nagwa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Pamene adani ndi amaliwongo anga andiputa kuti andiphe, adzaphunthwa ndipo adzagwa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Pamene anthu oyipa abwera kudzalimbana nane kudzadya mnofu wanga, pamene adani anga ndi achiwembu andithira nkhondo, iwo adzapunthwa ndi kugwa. Onani mutuwo |