Masalimo 139:15 - Buku Lopatulika15 Thupi langa silinabisikire Inu popangidwa ine mobisika, poombedwa ine monga m'munsi mwake mwa dziko lapansi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Thupi langa silinabisikira Inu popangidwa ine mobisika, poombedwa ine monga m'munsi mwake mwa dziko lapansi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Mapangidwe anga sadabisike pamaso panu pamene ndinkapangidwa mwachinsinsi, pamene ndinkaumbidwa mwaluso m'mimba mwa amai anga. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Mapangidwe anga sanabisike pamaso panu pamene ndimapangidwa mʼmalo achinsinsi, pamene ndinkawumbidwa mwaluso mʼmimba ya amayi anga. Onani mutuwo |