Masalimo 119:168 - Buku Lopatulika168 Ndinasamalira malangizo anu ndi mboni zanu; popeza njira zanga zonse zili pamaso panu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 2014168 Ndinasamalira malangizo anu ndi mboni zanu; popeza njira zanga zonse zili pamaso panu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa168 Ndimatsata malamulo anu ndi malangizo anu, pakuti makhalidwe anga onse mukuŵaona. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero168 Ndimamvera malangizo anu ndi umboni wanu, pakuti njira zanga zonse ndi zodziwika pamaso panu. Onani mutuwo |