Marko 9:6 - Buku Lopatulika6 Pakuti sanadziwe chimene adzayankha; chifukwa anachita mantha ndithu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Pakuti sanadziwe chimene adzayankha; chifukwa anachita mantha ndithu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Ankatero chifukwa chosoŵa chonena, pakuti iye ndi anzake aja anali atagwidwa ndi mantha aakulu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 (Iye sanadziwe choti anene, anali ndi mantha akulu). Onani mutuwo |