Marko 9:34 - Buku Lopatulika34 Koma iwo anakhala chete; pakuti anatsutsana wina ndi mnzake panjira, kuti, wamkulu ndani? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201434 Koma iwo anakhala chete; pakuti anatsutsana wina ndi mnzake panjira, kuti, wamkulu ndani? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa34 Ophunzirawo adangoti chete. Ndiye kuti zimene ankatsutsana panjirapo zinali zakuti wamkulu ndani pakati pao. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero34 Koma anakhala chete chifukwa ali mʼnjira amatsutsana za kuti wamkulu kuposa onse ndani. Onani mutuwo |