Marko 9:3 - Buku Lopatulika3 ndipo zovala zake zinakhala zonyezimira, zoyera mbuu; monga ngati muomba wotsuka nsalu padziko lapansi sangathe kuziyeretsai. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 ndipo zovala zake zinakhala zonyezimira, zoyera mbu; monga ngati muomba wotsuka nsalu pa dziko lapansi sangathe kuziyeretsai. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Zovala zake zidasanduka zoŵala ndi zoyera kuti mbee, kupambana m'mene mmisiri wina aliyense angayeretsere nsalu pansi pano. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Zovala zake zinawala monyezimira kwambiri, kotero kuti palibe sopo wina aliyense amene angaziyeretse monyezimira chotere pa dziko la pansi. Onani mutuwo |