Marko 8:18 - Buku Lopatulika18 Pokhala nao maso simupenya kodi? Ndi pokhala nao makutu simukumva kodi? Ndipo simukumbukira kodi? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Pokhala nao maso simupenya kodi? Ndi pokhala nao makutu simukumva kodi? Ndipo simukumbukira kodi? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Maso muli nawo, kodi simuwona? Ndipo makutu muli nawo, kodi simumva? Kodi inu simukukumbukira zijazi? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Kodi muli ndi maso ndipo simukuona, ndi makutu ndipo mukulephera kumva? Kodi simukukumbukira? Onani mutuwo |