Marko 8:16 - Buku Lopatulika16 Ndipo anatsutsana wina ndi mnzake, nanena kuti, Tilibe mikate. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Ndipo anatsutsana wina ndi mnzake, nanena kuti, Tilibe mikate. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Apo ophunzirawo adayamba kukambirana nkumati, “Akuterotu chifukwa tilibe buledi.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Iwo anakambirana wina ndi mnzake ndipo anati, “Ndi chifukwa choti tilibe buledi.” Onani mutuwo |