Marko 4:16 - Buku Lopatulika16 Ndipo momwemonso iwo ndiwo amene afesedwa pathanthwe, atamva mau, awalandira pomwepo ndi kusekera; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Ndipo momwemonso iwo ndiwo amene afesedwa pathanthwe, atamva mau, awalandira pomwepo ndi kusekera; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Mbeu zofesedwa pa nthaka yamiyala zija zikutanthauza anthu amene amaŵamva mau a Mulungu, nthaŵi yomweyo nkuŵalandira ndi chimwemwe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Ena, monga mbewu zofesedwa pa miyala, amamva mawu ndipo nthawi yomweyo amawalandira ndi chimwemwe. Onani mutuwo |