Marko 3:30 - Buku Lopatulika30 pakuti adanena, Ali ndi mzimu wonyansa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201430 pakuti adanena, Ali ndi mzimu wonyansa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa30 Yesu adalankhula zimenezi poona kuti anthu aja ankanena kuti, “Wagwidwa ndi mzimu woipa.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero30 Ananena izi chifukwa anati, “Ali ndi mzimu woyipa.” Onani mutuwo |