Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Marko 14:57 - Buku Lopatulika

57 Ndipo ananyamukapo ena, namchitira umboni wakunama, nanena kuti,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

57 Ndipo ananyamukapo ena, namchitira umboni wakunama, nanena kuti,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

57 Ena adaimirira nayamba kumneneza zabodza.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

57 Kenaka ena anayimirira namunenera umboni wonama womutsutsa Iye kunena kuti,

Onani mutuwo Koperani




Marko 14:57
9 Mawu Ofanana  

Mika Mmoreseti ananenera masiku a Hezekiya mfumu ya Yuda; ndipo iye ananena kwa anthu onse a Yuda, kuti, Yehova wa makamu atero: Ziyoni adzalimidwa ngati munda, Yerusalemu adzakhala miunda, ndi phiri la nyumba longa misanje ya nkhalango.


nati, Nanga Iwe, wopasula Kachisi, ndi kummanganso masiku atatu, tadzipulumutsa wekha; ngati uli Mwana wa Mulungu, tatsika pamtandapo.


Pakuti ambiri anamchitira umboni wonama, ndipo umboni wao sunalingane.


Ife tinamva Iye alikunena, kuti, Ine ndidzaononga Kachisi uyu wopangidwa ndi manja, ndi masiku atatu ndidzamanga wina wosapangidwa ndi manja.


Ndipo iwo akupitirirapo anamchitira mwano, napukusa mitu yao, nanena, Ha! Iwe wakupasula Kachisi, ndi kummanga masiku atatu,


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa