Marko 13:1 - Buku Lopatulika1 Ndipo pamene analikutuluka Iye mu Kachisi, mmodzi wa ophunzira ake ananena kwa Iye, Mphunzitsi, onani, miyala yotere ndi nyumba yotere. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Ndipo pamene analikutuluka Iye m'Kachisi, mmodzi wa ophunzira ake ananena kwa Iye, Mphunzitsi, onani, miyala yotere ndi nyumba yotere. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Pamene Yesu ankachoka ku Nyumba ya Mulungu, wophunzira wake wina adamuuza kuti, “Aphunzitsi, taonani kukongola kwake miyalayi ndi nyumbazi.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Iye atachoka mʼNyumba ya Mulungu, mmodzi wa ophunzira ake anati kwa Iye, “Aphunzitsi taonani! Miyala ikuluikulu! Nyumba zikongolerenji!” Onani mutuwo |