Marko 1:19 - Buku Lopatulika19 Ndipo atapita patsogolo pang'ono, anaona Yakobo, mwana wa Zebedeo, ndi Yohane mbale wake, iwonso anali m'chombo nakonza makoka ao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 Ndipo atapita patsogolo pang'ono, anaona Yakobo, mwana wa Zebedeo, ndi Yohane mbale wake, iwonso anali m'chombo nakonza makoka ao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 Atapitirira pang'ono, Yesu adaona Yakobe ndi Yohane, ana a Zebedeo. Iwowo anali m'chombo, akukonza makoka ao, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 Atapita patsogolo pangʼono, anaona Yakobo ndi mʼbale wake Yohane ana a Zebedayo, ali mʼbwato akukonza makoka awo. Onani mutuwo |