Marko 1:13 - Buku Lopatulika13 Ndipo anakhala m'chipululu masiku makumi anai woyesedwa ndi Satana; nakhala ndi zilombo, ndipo angelo anamtumikira. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Ndipo anakhala m'chipululu masiku makumi anai woyesedwa ndi Satana; nakhala ndi zilombo, ndipo angelo anamtumikira. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Yesuyo adakhala kumeneko masiku makumi anai, Satana akumuyesa. Komweko kunalinso nyama zakuthengo, ndipo angelo ankamutumikira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 ndipo anali mʼchipululumo masiku makumi anayi, akuyesedwa ndi Satana. Anali pakati pa nyama zakuthengo; ndipo angelo anamutumikira. Onani mutuwo |