Machitidwe a Atumwi 27:3 - Buku Lopatulika3 Ndipo m'mawa mwake tinangokocheza ku Sidoni; ndipo Julio anachitira Paulo mwachikondi, namlola apite kwa abwenzi ake amchereze. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Ndipo m'mawa mwake tinangokocheza ku Sidoni; ndipo Julio anachitira Paulo mwachikondi, namlola apite kwa abwenzi ake amchereze. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 M'maŵa mwake tidafika ku Sidoni, ndipo Julio adakomera mtima Paulo, namlola kupita kwa abwenzi ake kuti akamsamale. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Mmawa mwake tinafika ku Sidoni; ndipo Yuliyo, mokomera mtima Paulo, anamulola kupita kwa abwenzi ake kuti akamupatse zosowa zake. Onani mutuwo |