Machitidwe a Atumwi 2:3 - Buku Lopatulika3 Ndipo anaonekera kwa iwo malilime ogawanikana, onga amoto; ndipo unakhala pa iwo onse wayekhawayekha. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Ndipo anaonekera kwa iwo malilime ogawanikana, onga amoto; ndipo unakhala pa iwo onse wayekhawayekha. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Ndipo adaona ngati timalaŵi ta moto tooneka ngati malilime tikugaŵikana nkukhala pa iwo, aliyense kakekake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Iwo anaona zinthu zokhala ngati malilime amoto ogawikana ndipo anakhala pa aliyense wa iwo. Onani mutuwo |