Machitidwe a Atumwi 18:3 - Buku Lopatulika3 ndipo popeza anali wa ntchito imodzimodzi, anakhala nao, ndipo iwowa anagwira ntchito; pakuti ntchito yao inali yakusoka mahema. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 ndipo popeza anali wa ntchito imodzimodzi, anakhala nao, ndipo iwowa anagwira ntchito; pakuti ntchito yao inali yakusoka mahema. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Ndiye popeza kuti iwo anali amisiri a ntchito imodzimodzi ngati yake, yosoka mahema, iyeyo adakhala nawo namagwirira limodzi ntchito. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Popeza Paulo anali mʼmisiri wosoka matenti monga iwo, iye anakhala nawo namagwirira ntchito pamodzi. Onani mutuwo |