Luka 9:17 - Buku Lopatulika17 Ndipo anadya, nakhuta onsewo; natola makombo, madengu khumi ndi awiri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Ndipo anadya, nakhuta onsewo; natola makombo, madengu khumi ndi awiri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Anthu onse aja adadya nakhuta. Ndipo ophunzira aja adatola zotsala, nkudzaza madengu khumi ndi aŵiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Onse anadya nakhuta, ndipo ophunzira ake anatolera madengu khumi ndi awiri odzaza ndi nyenyeswa zomwe zinatsala. Onani mutuwo |