Luka 8:4 - Buku Lopatulika4 Ndipo pamene khamu lalikulu la anthu linasonkhana, ndi anthu a kumidzi yonse anafika kwa Iye, anati mwa fanizo: Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Ndipo pamene khamu lalikulu la anthu linasonkhana, ndi anthu a kumidzi yonse anafika kwa Iye, anati mwa fanizo: Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Anthu ambirimbiri ochokera ku midzi yonse adasonkhana kumene kunali Yesu. Tsono Iye adaŵaphera fanizo. Adati, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Anthu ambiri ankasonkhana, ndipo pamene anthu ankabwera kwa Yesu kuchokera ku midzi, Iye anawawuza fanizo ili, Onani mutuwo |