Luka 8:36 - Buku Lopatulika36 Ndipo amene anaona anawauza iwo machiritsidwe ake a wogwidwa chiwandayo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201436 Ndipo amene anaona anawauza iwo machiritsidwe ake a wogwidwa chiwandayo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa36 Anzao amene adaaonerera zonse zikuchitika, adaŵasimbira m'mene munthu wamizimuyo adaamchiritsira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero36 Amene anaona izi anawuza anthu mmene munthu wogwidwa ndi ziwandayo anachiritsidwira. Onani mutuwo |