Luka 5:34 - Buku Lopatulika34 Koma Yesu anati kwa iwo, Kodi mungathe kuletsa anyamata a ukwati asadye, pamene mkwati ali nao pamodzi? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201434 Koma Yesu anati kwa iwo, Kodi mungathe kuletsa anyamata a ukwati asadye, pamene mkwati ali nao pamodzi? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa34 Yesu adati, “Kani anzake a mkwati angathe kumasala zakudya pamene mkwati ali nao pomwepo? Chosatheka! Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero34 Yesu anawayankha kuti, “Kodi alendo a mkwati angasale kudya pamene mkwati ali pakati pawo? Onani mutuwo |