Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Luka 5:11 - Buku Lopatulika

11 Ndipo m'mene iwo anakocheza ngalawa zao pamtunda, anasiya zonse, namtsata Iye.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

11 Ndipo m'mene iwo anakocheza ngalawa zao pamtunda, anasiya zonse, namtsata Iye.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

11 Motero, atakokera zombozo ku mtunda, adasiya zonse namatsata Yesu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

11 Kenaka anakokera mabwato awo ku mtunda, nasiya zonse namutsata Iye.

Onani mutuwo Koperani




Luka 5:11
11 Mawu Ofanana  

Iye wakukonda atate wake, kapena amake koposa Ine, sayenera Ine, ndipo iye wakukonda mwana wake wamwamuna, kapena wamkazi koposa Ine, sayenera Ine.


Pomwepo Petro anayankha, nati kwa Iye, onani, ife tinasiya zonse ndi kutsata Inu; nanga tsono tidzakhala ndi chiyani?


Ndipo onse amene adasiya nyumba, kapena abale, kapena alongo, kapena atate, kapena amai, kapena ana, kapena minda, chifukwa cha dzina langa, adzalandira zobwezeredwa zambirimbiri, nadzalowa moyo wosatha.


Ndipo iwo anasiya pomwepo makokawo, namtsata Iye.


Ndipo anasiya pomwepo ngalawayo ndi atate wao, namtsata Iye.


Ndipo Yesu anamyang'ana, namkonda, nati kwa iye, Chinthu chimodzi chikusowa: pita, gulitsa zonse uli nazo, nuzipereke kwa anthu aumphawi, ndipo chuma udzakhala nacho m'mwamba; ndipo ukadze kuno, unditsate Ine.


Ndipo iye anasiya zonse, nanyamuka, namtsata Iye.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa