Luka 4:30 - Buku Lopatulika30 Koma Iye anapyola pakati pao, nachokapo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201430 Koma Iye anapyola pakati pao, nachokapo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa30 koma Iye adangodzadutsa pakati pao, nkumapita. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero30 Koma Iye anangoyenda pakati pa gulu la anthulo nachokapo. Onani mutuwo |