Luka 3:10 - Buku Lopatulika10 Ndipo anthu a makamu anamfunsa iye, nanena, Ndipo tsono tizichita chiyani? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Ndipo anthu a makamu anamfunsa iye, nanena, Ndipo tsono tizichita chiyani? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Pamenepo anthu aja adafunsa Yohane kuti, “Tsono ife tizichita zabwino zanji?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Gulu la anthuwo linafunsa kuti, “Nanga tsono tichite chiyani?” Onani mutuwo |