Luka 24:9 - Buku Lopatulika9 nabwera kuchokera kumanda, nafotokozera zonse khumi ndi mmodziwo, ndi otsala onse omwe. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 nabwera kuchokera kumanda, nafotokozera zonse khumi ndi mmodziwo, ndi otsala onse omwe. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 ndipo atabwerako kumanda kuja, adasimbira zonsezo ophunzira khumi ndi mmodzi aja, ndi anthu ena onse. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Atabwerera kuchokera ku mandako, anafotokoza zinthu zonse kwa khumi ndi mmodziwo ndi kwa ena onse. Onani mutuwo |