Luka 20:8 - Buku Lopatulika8 Ndipo Yesu anati kwa iwo Ndingakhale Inenso sindikuuzani ulamuliro umene ndichita nao zinthu izi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Ndipo Yesu anati kwa iwo Ndingakhale Inenso sindikuuzani ulamuliro umene ndichita nao zinthu izi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Apo Yesu adati, “Nanenso tsono sindikuuzani kumene ndidazitenga mphamvu zoti ndizichita zimenezi.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Yesu anati, “Ngakhale Inenso sindikuwuzani kuti ndi ulamuliro wanji umene ndikuchitira zimenezi.” Onani mutuwo |