Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Luka 20:34 - Buku Lopatulika

34 Ndipo Yesu anati kwa iwo, Ana a dziko lapansi akwatira nakwatiwa:

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

34 Ndipo Yesu anati kwa iwo, Ana a dziko lapansi akwatira nakwatiwa:

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

34 Yesu adaŵayankha kuti, “Anthu okhala pansi pano amakwatira ndi kukwatiwa.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

34 Yesu anayankha kuti, “Anthu a mʼbado uno amakwatira ndi kukwatiwa.

Onani mutuwo Koperani




Luka 20:34
7 Mawu Ofanana  

Ndipo aliyense amene anganenere Mwana wa Munthu zoipa, adzakhululukidwa; koma aliyense amene anganenere Mzimu Woyera zoipa sadzakhululukidwa nthawi ino kapena ilinkudzayo.


Ndipo mbuye wake anatama kapitao wonyengayo, kuti anachita mwanzeru; chifukwa ana a nthawi ya pansi pano ali anzeru m'mbadwo wao koposa ana a kuunika.


Anadya, anamwa, anakwatira, anakwatiwa, kufikira tsiku lija Nowa analowa m'chingalawa, ndipo chinadza chigumula, nkuwaononga onsewo.


Potero m'kuuka iye adzakhala mkazi wa yani wa iwo? Pakuti asanu ndi awiriwo adamkwatira iye.


Chifukwa cha ichi munthu azisiya atate ndi amai, nadzaphatikizana ndi mkazi wake; ndipo iwo awiri adzakhala thupi limodzi.


Ukwati uchitidwe ulemu ndi onse, ndi pogona pakhale posadetsedwa; pakuti adama ndi achigololo adzawaweruza Mulungu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa