Luka 18:6 - Buku Lopatulika6 Ndipo Ambuye anati, Tamverani chonena woweruza wosalungama. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Ndipo Ambuye anati, Tamverani chonena woweruza wosalungama. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Tsono Ambuye adati, “Mwamvatu mau a woweruza wosalungama uja. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Ndipo Ambuye anati, “Tamvani zimene woweruza wopanda chilungamoyu wanena. Onani mutuwo |