Luka 17:21 - Buku Lopatulika21 ndipo sadzanena, Taonani uwu, kapena uwo! Pakuti, taonani, Ufumu wa Mulungu uli m'kati mwa inu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 ndipo sadzanena, Taonani uwu, kapena uwo! Pakuti, taonani, Ufumu wa Mulungu uli m'kati mwa inu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Anthu sadzati, ‘Suuwu, uli pano,’ kapena, ‘Suuwo,’ pakuti ngakhale tsopano Mulungu akukhazikitsa ufumu wake pakati panu.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 kapenanso kuti anthu adzati, ‘Uwu uli apa,’ kapena ‘Uwo uli apo,’ Pakuti taonani ufumu wa Mulungu uli pakati panu.” Onani mutuwo |