Luka 15:11 - Buku Lopatulika11 Ndipo Iye anati, Munthu wina anali ndi ana aamuna awiri; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Ndipo Iye anati, Munthu wina anali ndi ana amuna awiri; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Yesu adatinso, “Munthu wina adaali ndi ana aamuna aŵiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Yesu anapitiriza kunena kuti, “Panali munthu amene anali ndi ana aamuna awiri. Onani mutuwo |