Luka 14:34 - Buku Lopatulika34 Kotero mchere uli wokoma; koma ngati mchere utasukuluka adzaukoleretsa ndi chiyani? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201434 Kotero mchere uli wokoma; koma ngati mchere utasukuluka adzaukoleretsa ndi chiyani? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa34 “Mchere ndi wabwino. Koma ngati mcherewo watha mphamvu, mphamvu zakezo nkuzibwezeranso nchiyani? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero34 “Mchere ndi wabwino, koma ngati usukuluka adzawukoleretsanso ndi chiyani? Onani mutuwo |