Luka 12:9 - Buku Lopatulika9 Koma iye wondikana Ine pamaso pa anthu, iye adzakanidwa pamaso pa angelo a Mulungu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Koma iye wondikana Ine pamaso pa anthu, iye adzakanidwa pamaso pa angelo a Mulungu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Koma aliyense wondikana pamaso pa anthu kuti sandidziŵa, Inenso Mwana wa Munthune ndidzamkana pamaso pa angelo a Mulungu kuti sindimdziŵa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Koma iye amene andikana Ine pamaso pa anthu adzakanidwanso pamaso pa angelo a Mulungu. Onani mutuwo |