Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Luka 11:30 - Buku Lopatulika

30 Pakuti monga ngati Yona anali chizindikiro kwa Aninive, chotero adzakhalanso Mwana wa Munthu kwa mbadwo uno.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

30 Pakuti monga ngati Yona anali chizindikiro kwa Aninive, chotero adzakhalanso Mwana wa Munthu kwa mbadwo uno.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

30 Monga Yona uja anali chizindikiro kwa anthu a ku Ninive, chomwechonso Mwana wa Munthu adzakhala chizindikiro kwa anthu a mbadwo uno.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

30 Monga Yona uja anali chizindikiro kwa anthu ku Ninive, momwemonso Mwana wa Munthu adzakhala chizindikiro kwa anthu a mʼbado uno.

Onani mutuwo Koperani




Luka 11:30
7 Mawu Ofanana  

Momwemo Ezekiele adzakhala kwa inu chizindikiro; umo monse anachitira iye mudzachita ndinu; chikadza ichi mudzadziwa kuti Ine ndine Ambuye Yehova.


Ndipo mau a Yehova anadza kwa Yona mwana wa Amitai, ndi kuti,


Koma Yehova anaikiratu chinsomba chachikulu chimeze Yona; ndipo Yona anali m'mimba mwa nsombayi masiku atatu usana ndi usiku.


Pamenepo Yehova analankhula ndi nsombayo, ndipo inamsanzira Yona kumtunda.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa