Luka 11:25 - Buku Lopatulika25 ndipo pofika, uipeza yosesa ndi yokonzeka. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201425 ndipo pofika, uipeza yosesa ndi yokonzeka. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa25 Tsono ukafika, umapeza m'nyumba muja muli mosesasesa ndi mokonza bwino. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero25 Ukafika umapeza mʼnyumba mosesedwa bwino ndi mokonza. Onani mutuwo |