Luka 10:4 - Buku Lopatulika4 Musanyamule thumba la ndalama kapena thumba la kamba, kapena nsapato; nimusalonjere munthu panjira. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Musanyamule thumba la ndalama kapena thumba la kamba, kapena nsapato; nimusalonjere munthu panjira. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Musatenge chikwama cha ndalama, kapena thumba lapaulendo, kapenanso nsapato zapadera ai. Musaimenso kuti mupereke moni pa njira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Musatenge chikwama kapena thumba kapena nsapato; ndipo musalonjere wina aliyense pa njira. Onani mutuwo |