Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Luka 10:26 - Buku Lopatulika

26 Ndipo anati kwa iye, M'chilamulo mulembedwa chiyani? Uwerenga bwanji?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

26 Ndipo anati kwa iye, M'chilamulo mulembedwa chiyani? Uwerenga bwanji?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

26 Yesu adati, “Kodi m'Malamulo mudalembedwa chiyani? Mumaŵerengamo zotani?”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

26 Yesu anayankha kuti, “Mwalembedwa chiyani mʼMalamulo, ndipo iwe umawerenga zotani?”

Onani mutuwo Koperani




Luka 10:26
8 Mawu Ofanana  

Kuchilamulo ndi kuumboni! Ngati iwo sanena malinga ndi mau awa, ndithu sadzaona mbandakucha.


Ndipo taonani, wachilamulo wina anaimirira namuyesa Iye, nanena, Mphunzitsi, ndidzalowa moyo wosatha ndi kuchita chiyani?


Ndipo iye anayankha nati, Uzikonda Ambuye Mulungu wako ndi mtima wako wonse, ndi moyo wako wonse, ndi mphamvu yako yonse, ndi nzeru zako zonse, ndi mnansi wako monga iwe mwini.


Pakuti Mose walemba kuti munthu amene achita chilungamo cha m'lamulo, adzakhala nacho ndi moyo.


Ndipo tidziwa kuti zinthu zilizonse chizinena chilamulo chizilankhulira iwo ali nacho chilamulo; kuti pakamwa ponse patsekedwe, ndi dziko lonse lapansi litsutsidwe ndi Mulungu;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa