Luka 10:23 - Buku Lopatulika23 Ndipo m'mene anapotolokera kwa ophunzira ake, ali pa okha, anati, Odala masowo akuona zimene muona. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 Ndipo m'mene anapotolokera kwa ophunzira ake, ali pa okha, anati, Odala masowo akuona zimene muona. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 Pambuyo pake Yesu adatembenukira ophunzira ake, naŵauza iwo okha kuti, “Ngodala maso amene akuwona zimene mukuwonazi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 Kenaka anatembenukira kwa ophunzira ake nawawuza iwo okha kuti, “Ndi odala maso amene akuona zimene mukuonazi. Onani mutuwo |