Luka 1:7 - Buku Lopatulika7 Ndipo analibe mwana, popeza Elizabeti anali wouma, ndipo onse awiri anakalamba. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Ndipo analibe mwana, popeza Elizabeti anali wouma, ndipo onse awiri anakalamba. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Adaalibe mwana, chifukwa Elizabeti anali wosabala, ndipo aŵiri onsewo anali okalamba. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Koma analibe ana chifukwa Elizabeti anali wosabereka; ndipo onse anali okalamba. Onani mutuwo |