Luka 1:19 - Buku Lopatulika19 Ndipo mngelo anayankha, nati kwa iye, Ine ndine Gabriele, woimirira pamaso pa Mulungu; ndipo ndinatumidwa kwa iwe kudzalankhula nawe, ndi kuuza iwe uthenga uwu wabwino. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 Ndipo mngelo anayankha, nati kwa iye, Ine ndine Gabriele, woimirira pamaso pa Mulungu; ndipo ndinatumidwa kwa iwe kudzalankhula nawe, ndi kuuza iwe uthenga uwu wabwino. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 Mngeloyo adati, “Ine ndine Gabriele, amene ndimakhala kufupi ndi Mulungu. Iyeyo wachita kundituma kuti ndilankhule nawe ndi kukuuza uthenga wabwinowu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 Mngeloyo anayankha kuti, “Ine ndine Gabrieli. Ndimayima pamaso pa Mulungu, ndipo ndatumidwa kwa iwe kudzakuwuza uthenga wabwinowu. Onani mutuwo |