Levitiko 6:3 - Buku Lopatulika3 kapena anapeza chinthu chotayika, nanenapo bodza, nalumbira pabodza; pa chimodzi cha izi zonse amachita munthu, ndi kuchimwapo; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 kapena anapeza chinthu chotayika, nanenapo bodza, nalumbira pabodza; pa chimodzi cha izi zonse amachita munthu, ndi kuchimwapo; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 kapena kunama kuti sadatole zimene zidatayika, kapena kumalumbira zonama pa kanthu kalikonse, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 kapena ndi kunama kuti sanatole chinthu chimene chinatayika, kapena kulumbira mwachinyengo pa chinthu chilichonse chimene munthu akachita amachimwa nacho, Onani mutuwo |