Levitiko 11:9 - Buku Lopatulika9 Mwa zonse zili m'madzi muyenera kumadya izi: zilizonse zili nazo zipsepse ndi mamba m'madzi, m'nyanja, ndi m'mitsinje, zimenezo muyenera kumadya. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Mwa zonse zili m'madzi muyenera kumadya izi: zilizonse zili nazo zipsepse ndi mamba m'madzi, m'nyanja, ndi m'mitsinje, zimenezo muyenera kumadya. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 “Zamoyo zam'madzi zimene mutha kudya ndi izi: zonse zam'madzi zimene zili ndi zilimba ndi mamba, mungathe kudya, ngakhale zikhale zam'nyanja kapena zam'mitsinje. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 “ ‘Mwa zamoyo zonse zimene zimakhala mʼmadzi a mʼnyanja ndi a mʼmitsinje mukhoza kudya chilichonse chimene chili ndi minga ya pa msana ndi mamba. Onani mutuwo |