Levitiko 11:10 - Buku Lopatulika10 Koma zilizonse zilibe zipsepse ndi mamba m'nyanja, ndi m'mitsinje, mwa zonse zokwawa za m'madzi, ndi mwa zamoyo zonse zili m'madzi, muziziyesa zonyansa; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Koma zilizonse zilibe zipsepse ndi mamba m'nyanja, ndi m'mitsinje, mwa zonse zokwawa za m'madzi, ndi mwa zamoyo zonse zili m'madzi, muziziyesa zonyansa; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Koma zamoyo zonse zam'nyanja kapena zam'mitsinje zopanda zilimba ndi mamba, tizilombo tonse tam'madzi ndi zamoyo zonse zopezeka m'menemo, nzonyansa kwa inu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Koma zamoyo zonse za mʼnyanja kapena za mʼmitsinje zimene zilibe minga ya pa msana ndi mamba, kaya ndi tizirombo tonse ta mʼmadzi ndi zamoyo zonse zopezeka mʼmenemo ndi zodetsedwa kwa inu. Onani mutuwo |