Hoseya 4:11 - Buku Lopatulika11 Chigololo, ndi vinyo, ndi vinyo watsopano, zichotsa mtima. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Chigololo, ndi vinyo, ndi vinyo watsopano, zichotsa mtima. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Chauta akuti, “Vinyo, kaya ndi wakale kaya ndi watsopano, amaononga nzeru. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 ku zachiwerewere, ku vinyo wakale ndi watsopano, zimene zimachotsa nzeru zomvetsa zinthu Onani mutuwo |