Hoseya 2:3 - Buku Lopatulika3 ndingamvule wamaliseche, ndi kumuika ngati tsiku lija anabadwalo, ndi kumsanduliza ngati chipululu, ndi kumuika ngati dziko louma, ndi kumupha nalo ludzu; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 ndingamvule wamaliseche, ndi kumuika ngati tsiku lija anabadwalo, ndi kumsanduliza ngati chipululu, ndi kumuika ngati dziko louma, ndi kumupha nalo ludzu; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Akapanda kutero ndimuvula, kuti akhale monga momwe adabadwira. Ndidzamuumitsa ngati chipululu, adzakhala ngati dziko lopanda madzi, ndidzamphetsa ndi ludzu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Akapanda kutero ndidzamuvula, ndipo adzakhala wamaliseche monga tsiku limene anabadwa; ndidzamuwumitsa ngati chipululu, adzakhala ngati dziko lopanda madzi, ndi kumupha ndi ludzu. Onani mutuwo |