Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Hoseya 1:5 - Buku Lopatulika

5 Ndipo kudzachitika tsiku lomwelo, ndidzathyola uta wa Israele m'chigwa cha Yezireele.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

5 Ndipo kudzachitika tsiku lomwelo, ndidzathyola uta wa Israele m'chigwa cha Yezireele.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

5 Nthaŵi imeneyo ndidzathetsa mphamvu za Israele m'chigwa cha Yezireele.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

5 Tsiku limenelo ndidzathyola uta wa Israeli mʼchigwa cha Yezireeli.”

Onani mutuwo Koperani




Hoseya 1:5
9 Mawu Ofanana  

Masiku a Peka mfumu ya Israele anadza Tigilati-Pilesere mfumu ya Asiriya, nalanda Iyoni, ndi Abele-Beti-Maaka, ndi Yanowa, ndi Kedesi, ndi Hazori, ndi Giliyadi, ndi Galileya, dziko lonse la Nafutali; nawatenga andende kunka nao ku Asiriya.


Lupanga lao lidzalowa m'mtima mwao momwe, ndipo mauta ao adzathyoledwa.


Aletsa nkhondo ku malekezero a dziko lapansi; athyola uta, nadula nthungo; atentha magaleta ndi moto.


pakuti wakufunkha wafika kwa iye, kwa Babiloni, ndi anthu ake olimba agwidwa, mauta ao athyokathyoka, pakuti Yehova ndiye Mulungu wakubwezera, adzabwezera ndithu.


ndipo ndidzakantha uta wako kuuchotsa m'dzanja lako lamanzere, ndi kutayitsa mivi yako kudzanja lako lamanja.


Ndipo tsiku lomwelo ndidzawachitira pangano ndi nyama zakuthengo, ndi mbalame za mlengalenga, ndi zokwawa pansi; ndipo ndidzathyola uta, ndi lupanga, ndi nkhondo, zichoke m'dziko, ndi kuwagonetsa pansi mosatekeseka.


Ndipo ana a Yosefe anati, Ku phiriko sikudzatifikira; ndipo Akanani onse akukhala m'dziko la chigwa ali nao magaleta achitsulo, iwo akukhala mu Beteseani, ndi midzi yake ndi iwo omwe akukhala m'chigwa cha Yezireele.


Pamenepo Amidiyani onse ndi Aamaleke ndi ana a kum'mawa anasonkhana pamodzi naoloka, namanga misasa m'chigwa cha Yezireele.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa