Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Hoseya 1:3 - Buku Lopatulika

3 Ndipo anamuka natenga Gomeri mwana wamkazi wa Dibulaimu; iye naima, nambalira mwana wamwamuna.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

3 Ndipo anamuka natenga Gomeri mwana wamkazi wa Dibulaimu; iye naima, nambalira mwana wamwamuna.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

3 Motero Hoseya adapita, nakakwatira mkazi, dzina lake Gomeri, mwana wa Dibulaimu. Mkaziyo adatenga pathupi, namubalira mwana wamwamuna.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

3 Motero Hoseya anakwatira Gomeri mwana wamkazi wa Dibulaimu, ndipo mkaziyo anakhala woyembekezera nabala mwana wamwamuna.

Onani mutuwo Koperani




Hoseya 1:3
3 Mawu Ofanana  

Ndipo mwamunayo anadziwa mkazi wake Heva: ndipo anatenga pakati, nabala Kaini, ndipo anati, Ndalandira munthu kwa Yehova.


Ndipo maina ao ndiwo Ohola wamkulu, ndi Oholiba mng'ono wake; nakhala anga, nabala ana aamuna ndi aakazi. Ndipo maina ao, Samariya ndiye Ohola, ndi Yerusalemu ndiye Oholiba.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa