Genesis 9:14 - Buku Lopatulika14 Ndipo padzakhala pophimba ndi mtambo Ine dziko lapansi, utawo udzaoneka m'mtambomo; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Ndipo padzakhala pophimba ndi mtambo Ine dziko lapansi, utawo udzaoneka m'mtambomo; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Nthaŵi zonse pakakhala mitambo mu mlengalenga, ndipo pakaoneka utawaleza m'mitambomo, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Nthawi zonse pakakhala mitambo mu mlengalenga ndipo utawaleza uwoneka, Onani mutuwo |