Genesis 9:12 - Buku Lopatulika12 Ndipo anati Mulungu, Ichi ndi chizindikiro cha pangano limene ndipangana ndi Ine ndi inu, ndi zamoyo zonse zili pamodzi ndi inu, ku mibadwomibadwo; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Ndipo anati Mulungu, Ichi ndichi chizindikiro cha pangano limene ndipangana ndi Ine ndi inu, ndi zamoyo zonse zili pamodzi ndi inu, ku mibadwomibadwo; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Ndipo Mulungu adati, “Nachi chizindikiro cha chipangano chamuyaya chimene ndikuchiika pakati pa Ine ndi inu ndi cholengedwa chilichonse chimene chili ndi inu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Ndipo Mulungu anati, “Ine ndikupereka chizindikiro ichi cha pangano langa la pakati pa Ine ndi iwe, ana ako, zamoyo zonse, pamodzi ndi mibado ya mʼtsogolo. Onani mutuwo |